Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “M’bale wako, amene ndi mwana wamwamuna wa mayi ako, kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, mkazi wako wokondedwa kapena bwenzi lako lapamtima,+ akayesa kukupatutsa mwamseri pokuuza kuti, ‘Tiye tikatumikire milungu ina,’+ milungu imene iwe kapena makolo ako sanaidziwe,

  • Deuteronomo 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma umuphe ndithu.+ Dzanja lako lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+

  • 1 Mafumu 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aisiraeli onse ataona kuti mfumuyo sinawamvere, anaiyankha kuti: “Tili ndi gawo lanji mwa Davide?+ Ife tilibe cholowa mwa mwana wa Jese. Pitani kwa milungu yanu+ Aisiraeli. Tsopano iwe Davide,+ uzisamalira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, anayamba kubwerera kumahema awo.

  • 2 Mbiri 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Popeza kuti mfumuyo sinawamvere Aisiraeli onsewo, iwo anayankha mfumuyo kuti: “Tili ndi gawo lanji mwa Davide?+ Ife tilibe cholowa mwa mwana wa Jese.+ Aisiraeli inu, aliyense apite kwa milungu yake!+ Tsopano iwe Davide,+ uzisamalira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, onse anayamba kubwerera kumahema awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena