Oweruza 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atafika kumeneko anayamba kuliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa m’dera lamapiri la Efuraimu.+ Iye ali patsogolo, ana a Isiraeli anatsika naye limodzi kuchoka m’dera lamapirilo. 2 Samueli 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape+ m’mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, munene kuti, ‘Abisalomu wakhala mfumu+ ku Heburoni!’”+
27 Atafika kumeneko anayamba kuliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa m’dera lamapiri la Efuraimu.+ Iye ali patsogolo, ana a Isiraeli anatsika naye limodzi kuchoka m’dera lamapirilo.
10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape+ m’mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, munene kuti, ‘Abisalomu wakhala mfumu+ ku Heburoni!’”+