Yobu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi? Salimo 73:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi, mwawaimika pamalo oterera.+Mwawagwetsa kuti awonongeke.+ Mika 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+ Mateyu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense wodzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense wodzichepetsa adzakwezedwa.+
5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi?
6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+