-
2 Samueli 20:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Nkhani sili choncho ayi, koma mumzinda wanu muli munthu wochokera kudera lamapiri la Efuraimu,+ dzina lake Sheba+ mwana wa Bikiri, amene waukira Mfumu Davide.+ Choncho anthu inu m’perekeni iye yekhayo+ m’manja mwathu, ndipo ine ndidzachoka kumzinda+ uno.” Pamenepo mkaziyo anauza Yowabu kuti: “Tikuponyerani mutu+ wake kuchokera pamwamba pa mpanda!”
-