Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.” Oweruza 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
9 Ndipo anamuika m’manda ku Timinati-heresi,*+ m’dera limene analandira monga cholowa chake, m’dera lamapiri la Efuraimu, kumpoto kwa phiri la Gaasi.+