1 Samueli 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano anthuwo anayamba kuuza Samueli kuti: “Ndani akunena kuti, ‘Sauli sangakhale mfumu yathu?’+ Tipatseni anthu amenewo tiwaphe.”+ Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
12 Tsopano anthuwo anayamba kuuza Samueli kuti: “Ndani akunena kuti, ‘Sauli sangakhale mfumu yathu?’+ Tipatseni anthu amenewo tiwaphe.”+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+