1 Mafumu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+ 2 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehosafati anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero waukulu,+ koma anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Ahabu.+
27 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+
18 Yehosafati anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero waukulu,+ koma anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Ahabu.+