1 Mafumu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu ufumu wa Isiraeli mpaka kalekale, monga momwe ndinalonjezera Davide bambo ako kuti, ‘Munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+ Salimo 132:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+
5 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu ufumu wa Isiraeli mpaka kalekale, monga momwe ndinalonjezera Davide bambo ako kuti, ‘Munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+
12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+