Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali m’mbuyo mwathumu.’”+ Popeza mumtima mwake anati: “Mwina ndingamusangalatse potsogoza mphatsoyi,+ ndipo pambuyo pake ndingathe kuonana naye pamasom’pamaso, kuti mwina angandilandire bwino.”+

  • 2 Samueli 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Davide atapitirira pang’ono pamwamba pa phiri paja,+ anaona Ziba+ mtumiki wa Mefiboseti+ akubwera kudzakumana naye. Iye anali ndi abulu awiri+ okhala ndi zishalo ndipo abuluwa anali atanyamula mitanda 200 ya mkate,+ mphesa zouma zoumba pamodzi 100,+ zipatso za m’chilimwe* 100+ zouma zoumba pamodzi ndiponso mtsuko waukulu wa vinyo.+

  • Miyambo 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mphatso ya munthu imam’tsegulira khomo lalikulu,+ ndipo imakam’fikitsa ngakhale pamaso pa anthu olemekezeka.+

  • Miyambo 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu amene amakhazika pansi mtima wa munthu wolemekezeka ndi ambiri,+ ndipo aliyense amakhala bwenzi la munthu wopereka mphatso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena