Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 40:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine ndikhala ku Mizipa+ kuno kuti ndizikuimirani kwa Akasidi amene adzabwera kwa ife. Koma inu, sonkhanitsani vinyo,+ zipatso za m’chilimwe* ndi mafuta ndi kuziika m’ziwiya zanu ndipo muzikhala m’mizinda imene mwaitenga kukhala yanu.”

  • Amosi 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, anandionetsa masomphenya awa: Ndinaona dengu la zipatso za m’chilimwe.*+

  • Mika 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsoka kwa ine,+ chifukwa ndakhala ngati munthu wanjala amene sanapeze zipatso kuti adye.+ Ndakhala ngati munthu amene sanapeze nkhuyu zoyambirira zimene anali kuzilakalaka, nthawi yokolola zipatso za m’chilimwe* ndi mphesa itatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena