Genesis 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye Isiraeli anati: “Pita ukaone ngati abale ako ali bwino limodzi ndi nkhosa. Kenako ubwere udzandiuze.”+ Chotero, anamuuza kuti anyamuke kuchigwa cha Heburoni+ ndipo iye analowera ku Sekemu.
14 Ndiye Isiraeli anati: “Pita ukaone ngati abale ako ali bwino limodzi ndi nkhosa. Kenako ubwere udzandiuze.”+ Chotero, anamuuza kuti anyamuke kuchigwa cha Heburoni+ ndipo iye analowera ku Sekemu.