Miyambo 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+ Miyambo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wochenjera amene waona tsoka amabisala.+ Koma anthu osadziwa zinthu amene amangopitabe amalangidwa.+
3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+
12 Wochenjera amene waona tsoka amabisala.+ Koma anthu osadziwa zinthu amene amangopitabe amalangidwa.+