Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aliyense amene anaopa mawu a Yehova pakati pa atumiki a Farao anaonetsetsa kuti ziweto zake ndi antchito ake athawira m’nyumba.+

  • Salimo 57:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+

      Pakuti ine ndathawira kwa inu.+

      Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+

  • Miyambo 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+

  • Yesaya 26:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+

  • Aheberi 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anachita zimenezo kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, zimene chifukwa cha zinthu zimenezo n’zosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe kwambiri, kuti tigwire mwamphamvu chiyembekezo+ chimene chaikidwa patsogolo pathu.

  • Aheberi 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mwa chikhulupiriro, Nowa+ atachenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zimene zinali zisanaoneke,+ anasonyeza kuopa Mulungu ndipo anamanga chingalawa+ kuti banja lake lipulumukiremo. Mwa chikhulupiriro chimenecho, anatsutsa dziko,+ ndipo anakhala wolandira cholowa cha chilungamo,+ chimene chimabwera ndi chikhulupiriro.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena