Ezara 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nditangomva nkhani imeneyi, ndinang’amba zovala zanga+ n’kuyamba kuzula tsitsi la m’mutu mwanga+ ndi ndevu zanga, ndipo ndinakhala pansi ndili wokhumudwa ndi wachisoni kwambiri.+
3 Nditangomva nkhani imeneyi, ndinang’amba zovala zanga+ n’kuyamba kuzula tsitsi la m’mutu mwanga+ ndi ndevu zanga, ndipo ndinakhala pansi ndili wokhumudwa ndi wachisoni kwambiri.+