2 Samueli 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno mfumu inayamba kubwerera kwawo ndipo inafika ku Yorodano. Pamenepo anthu a Yuda anafika ku Giligala+ kuti apite kukakumana ndi mfumu ndi kuiperekeza pamene inali kuwoloka mtsinje wa Yorodano.
15 Ndiyeno mfumu inayamba kubwerera kwawo ndipo inafika ku Yorodano. Pamenepo anthu a Yuda anafika ku Giligala+ kuti apite kukakumana ndi mfumu ndi kuiperekeza pamene inali kuwoloka mtsinje wa Yorodano.