2 Samueli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa,+ ndipo anthu onse anaima, moti sanapitirizenso kuthamangitsa Isiraeli. Iwo sanayambirenso kumenyana. 2 Samueli 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ kuti anthu abwerere, kusiya kuthamangitsa Isiraeli. Chotero Yowabu analetsadi anthuwo.
28 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa,+ ndipo anthu onse anaima, moti sanapitirizenso kuthamangitsa Isiraeli. Iwo sanayambirenso kumenyana.
16 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa+ kuti anthu abwerere, kusiya kuthamangitsa Isiraeli. Chotero Yowabu analetsadi anthuwo.