Ezekieli 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale kuti anatambasula dzanja lake+ povomereza lumbiro, iye wanyoza lumbiro+ limenelo mwa kuphwanya pangano. Iye wachita zinthu zonsezi ndipo sadzapulumuka.”’+
18 Ngakhale kuti anatambasula dzanja lake+ povomereza lumbiro, iye wanyoza lumbiro+ limenelo mwa kuphwanya pangano. Iye wachita zinthu zonsezi ndipo sadzapulumuka.”’+