2 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+
5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+