Genesis 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’chaka cha 14, Kedorelaomere anabwera limodzi ndi mafumu omwe anali naye. Iwo anagonjetsa Arefai ku Asiteroti-karanaimu,+ Azuzi ku Hamu, Aemi+ ku Save-kiriyataimu, 2 Samueli 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero, Isibi-benobi mmodzi wa mbadwa za Arefai,+ amene anali ndi mkondo wamkuwa wolemera+ masekeli 300,* amenenso anali ndi lupanga latsopano m’chiuno mwake, anaganiza zoti aphe Davide.
5 M’chaka cha 14, Kedorelaomere anabwera limodzi ndi mafumu omwe anali naye. Iwo anagonjetsa Arefai ku Asiteroti-karanaimu,+ Azuzi ku Hamu, Aemi+ ku Save-kiriyataimu,
16 Zitatero, Isibi-benobi mmodzi wa mbadwa za Arefai,+ amene anali ndi mkondo wamkuwa wolemera+ masekeli 300,* amenenso anali ndi lupanga latsopano m’chiuno mwake, anaganiza zoti aphe Davide.