1 Mbiri 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ndiye anali limodzi ndi Davide ku Pasi-damimu+ kumene Afilisiti anasonkhana kuti achite nawo nkhondo. Kumeneko kunali munda wodzaza ndi balere, ndipo anthu anali atathawa chifukwa choopa Afilisitiwo.+
13 Iye ndiye anali limodzi ndi Davide ku Pasi-damimu+ kumene Afilisiti anasonkhana kuti achite nawo nkhondo. Kumeneko kunali munda wodzaza ndi balere, ndipo anthu anali atathawa chifukwa choopa Afilisitiwo.+