1 Samueli 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Afilisiti+ anayamba kusonkhanitsa anthu a m’misasa yawo kuti akamenye nkhondo. Atasonkhana pamodzi ku Soko,+ m’dera la Yuda, anakamanga msasa pakati pa Soko ndi Azeka+ ku Efesi-damimu.+
17 Ndiyeno Afilisiti+ anayamba kusonkhanitsa anthu a m’misasa yawo kuti akamenye nkhondo. Atasonkhana pamodzi ku Soko,+ m’dera la Yuda, anakamanga msasa pakati pa Soko ndi Azeka+ ku Efesi-damimu.+