1 Samueli 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, Gadi+ mneneri anauza Davide kuti: “Usakhalenso m’malo ovuta kufikako. Uchokeko ndi kubwera m’dziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachokako ndi kulowa munkhalango ya Hereti. 1 Mbiri 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova analankhula kwa Gadi,+ wamasomphenya wa Davide+ kuti:
5 Patapita nthawi, Gadi+ mneneri anauza Davide kuti: “Usakhalenso m’malo ovuta kufikako. Uchokeko ndi kubwera m’dziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachokako ndi kulowa munkhalango ya Hereti.