1 Mbiri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.
29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.