Genesis 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako iye analankhula kwa Efuroni pamaso pa eni dzikowo kuti: “Ndimvere chonde. Ine ndigulabe malowo. Landira silivayu+ kuti ndikaike mkazi wanga kumeneko.”
13 Kenako iye analankhula kwa Efuroni pamaso pa eni dzikowo kuti: “Ndimvere chonde. Ine ndigulabe malowo. Landira silivayu+ kuti ndikaike mkazi wanga kumeneko.”