Genesis 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikulumbira kuti pa zinthu zako sinditengapo kanthu n’kamodzi komwe,+ kaya kakhale kaulusi kapena kachingwe komangira nsapato. Ayi sinditero, kuti usadzati, ‘Ndine ndinamulemeretsa Abulamu.’ Aroma 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+
23 Ndikulumbira kuti pa zinthu zako sinditengapo kanthu n’kamodzi komwe,+ kaya kakhale kaulusi kapena kachingwe komangira nsapato. Ayi sinditero, kuti usadzati, ‘Ndine ndinamulemeretsa Abulamu.’
8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+