2 Mafumu 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano magulu achifwamba a Asiriya+ anapita kudziko la Isiraeli komwe anakagwirako kamtsikana n’kupita nako kwawo.+ Kenako kamtsikanako kanayamba kutumikira mkazi wa Namani. 2 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita ndipo anapita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba+ a Asiriya sanabwerenso ku Isiraeli.
2 Tsopano magulu achifwamba a Asiriya+ anapita kudziko la Isiraeli komwe anakagwirako kamtsikana n’kupita nako kwawo.+ Kenako kamtsikanako kanayamba kutumikira mkazi wa Namani.
23 Chotero mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita ndipo anapita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba+ a Asiriya sanabwerenso ku Isiraeli.