2 Samueli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu inati: “Kodi palibe aliyense wotsala m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha kwa Mulungu.”+ Poyankha Ziba anauza mfumu kuti: “Alipo mwana wamwamuna wa Yonatani, wolumala mapazi.”+
3 Ndiyeno mfumu inati: “Kodi palibe aliyense wotsala m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha kwa Mulungu.”+ Poyankha Ziba anauza mfumu kuti: “Alipo mwana wamwamuna wa Yonatani, wolumala mapazi.”+