Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yonatani+ mwana wa Sauli anali ndi mwana wamwamuna wolumala mapazi.+ Mwanayu anali ndi zaka zisanu pamene kunabwera uthenga wa imfa ya Sauli ndi Yonatani kuchokera ku Yezereeli.+ Uthengawu utafika, mlezi wake anamunyamula ndi kuthawa naye. Pamene anali kuthawa mwamantha, mleziyo anagwetsa mwanayo ndipo analumala. Mwanayo dzina lake anali Mefiboseti.+

  • 2 Samueli 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho Mefiboseti anali kukhala mu Yerusalemu pakuti anali kudya patebulo la mfumu nthawi zonse.+ Iye anali wolumala mapazi.+

  • 2 Samueli 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Poyankha anati: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu+ ndinanena kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu wamkazi kuti ndikwerepo ndi kupita pamodzi ndi mfumu,’ pakuti ine mtumiki wanu ndine wolumala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena