-
2 Samueli 4:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Yonatani mwana wa Sauli+ anali ndi mwana wamwamuna wolumala mapazi.+ Mwanayu anali ndi zaka 5 pamene kunabwera uthenga wochokera ku Yezereeli+ wakuti Sauli ndi Yonatani afa. Uthengawu utafika, mayi amene ankamusamalira anamunyamula nʼkuyamba kuthawa. Pamene ankathawa mwamantha, mayiyo anagwetsa mwanayo ndipo analumala. Mwanayo dzina lake linali Mefiboseti.+
-