1 Samueli 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, pamene Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe amene anali ku Yezereeli.+ 1 Samueli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero Davide anadzuka m’mawa kwambiri+ pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye ndi kubwerera kudziko la Afilisiti m’mawa umenewo. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+
29 Ndiyeno Afilisiti+ anasonkhanitsa asilikali awo onse ku Afeki, pamene Aisiraeli anamanga msasa pafupi ndi kasupe amene anali ku Yezereeli.+
11 Chotero Davide anadzuka m’mawa kwambiri+ pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye ndi kubwerera kudziko la Afilisiti m’mawa umenewo. Koma Afilisitiwo anapita ku Yezereeli.+