Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+ Salimo 119:133 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Mwapondetsa mwamphamvu mapazi anga pa mawu anu,+Ndipo musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+
133 Mwapondetsa mwamphamvu mapazi anga pa mawu anu,+Ndipo musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+