Ekisodo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pofika pano ndikanatambasula kale dzanja langa ndi kukupha ndi mliri, iweyo ndi anthu ako, kukufafanizani padziko lapansi.+ Salimo 109:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+
15 Pofika pano ndikanatambasula kale dzanja langa ndi kukupha ndi mliri, iweyo ndi anthu ako, kukufafanizani padziko lapansi.+
15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+