2 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+ 2 Samueli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthawi yonse imene Davide anakhala mfumu ku Heburoni, kulamulira nyumba ya Yuda, inali zaka 7 ndi miyezi 6.+
2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+
11 Nthawi yonse imene Davide anakhala mfumu ku Heburoni, kulamulira nyumba ya Yuda, inali zaka 7 ndi miyezi 6.+