Salimo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe anthu odzitama amene angaime pamaso panu.+Mumadana ndi onse ochita zopweteka ena.+