1 Mbiri 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anafika kumalo opunthira mbewu a Kidoni,+ ndipo Uza anatambasulira dzanja lake pa Likasa+ n’kuligwira, chifukwa ng’ombe zinatsala pang’ono kuligwetsa.
9 Kenako anafika kumalo opunthira mbewu a Kidoni,+ ndipo Uza anatambasulira dzanja lake pa Likasa+ n’kuligwira, chifukwa ng’ombe zinatsala pang’ono kuligwetsa.