2 Samueli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anafika kumalo opunthira mbewu a ku Nakoni, ndipo Uza+ anatambasulira dzanja lake pa likasa la Mulungu woona n’kuligwira,+ chifukwa ng’ombe zinatsala pang’ono kuligwetsa.
6 Kenako anafika kumalo opunthira mbewu a ku Nakoni, ndipo Uza+ anatambasulira dzanja lake pa likasa la Mulungu woona n’kuligwira,+ chifukwa ng’ombe zinatsala pang’ono kuligwetsa.