Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Aroni ndi ana ake akamaliza kuphimba zinthu za m’malo oyera+ ndi ziwiya zonse+ za m’malo oyerawo posamutsa msasa, ana a Kohati azilowamo n’kudzazinyamula.+ Iwo asamakhudze+ zinthu za m’malo oyerazo chifukwa angafe. Zinthu zimenezi ndizo katundu wa m’chihema chokumanako amene ana a Kohati azinyamula.+

  • Numeri 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kuti iwo asaphedwe poyandikira zinthu zopatulika koposa,+ koma akhalebe ndi moyo, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihemacho. Mmenemo azigawira aliyense wa iwo ntchito ndi katundu woti anyamule.

  • Numeri 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ana a Kohatiwo asadzayese kulowamo kuti akaone ngakhale pang’ono pokha zinthu zopatulikazo kuti angafe.”+

  • 1 Mbiri 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyi m’pamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndiwo ayenera kunyamula likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula likasa la Yehova+ ndi kum’tumikira+ mpaka kalekale.”*

  • Miyambo 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+

  • Miyambo 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena