Genesis 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pambuyo pake, Rubeni anabwerera kuchitsime kuja, koma anakapeza kuti Yosefe mulibe m’chitsimemo. Ataona choncho, anang’amba zovala zake.+ Numeri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+ Yoswa 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoswa ataona zimenezi anang’amba malaya ake. Kenako anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ patsogolo pa likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, n’kumadzithira fumbi kumutu kwawo.+
29 Pambuyo pake, Rubeni anabwerera kuchitsime kuja, koma anakapeza kuti Yosefe mulibe m’chitsimemo. Ataona choncho, anang’amba zovala zake.+
6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+
6 Yoswa ataona zimenezi anang’amba malaya ake. Kenako anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ patsogolo pa likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, n’kumadzithira fumbi kumutu kwawo.+