Deuteronomo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+ 2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+ Salimo 18:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndidzathamangitsa adani anga ndi kuwapeza,Ndipo sindidzabwerera kufikira nditawawononga onse.+
7 “Yehova adzachititsa adani ako amene adzakuukira kugonja pamaso pako.+ Pobwera kwa iwe adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pako, adzadutsa njira 7.+
22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+