1 Mbiri 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti inu Mulungu wanga mwandiululira ine mtumiki wanu cholinga chanu chondimangira nyumba,+ n’chifukwa chake ine mtumiki wanu ndapeza nthawi yopemphera pamaso panu. Salimo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+
25 Pakuti inu Mulungu wanga mwandiululira ine mtumiki wanu cholinga chanu chondimangira nyumba,+ n’chifukwa chake ine mtumiki wanu ndapeza nthawi yopemphera pamaso panu.
17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+