2 Samueli 22:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndidzaimbira Iye wochita ntchito zazikulu zachipulumutso kwa mfumu yake,+Iye wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.”+ Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+
51 Ndidzaimbira Iye wochita ntchito zazikulu zachipulumutso kwa mfumu yake,+Iye wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.”+
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+