1 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano mwamuna wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo tsiku limenelo, atang’amba zovala zake+ ndi kudzithira dothi kumutu.+
12 Tsopano mwamuna wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo tsiku limenelo, atang’amba zovala zake+ ndi kudzithira dothi kumutu.+