1 Mbiri 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli yense+ ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo kwa anthu ake onse.+ Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+ Miyambo 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mfumu ikamaweruza anthu onyozeka mwachilungamo,+ mpando wake wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.+
14 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli yense+ ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo kwa anthu ake onse.+
4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+
14 Mfumu ikamaweruza anthu onyozeka mwachilungamo,+ mpando wake wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.+