1 Mbiri 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mwana wa Yonatani anali Meribi-baala,+ ndipo Meribi-baala anabereka Mika.+ 1 Mbiri 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mwana wa Yonatani anali Meribi-baala,+ ndipo Meribi-baala anabereka Mika.+