Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yonatani+ mwana wa Sauli anali ndi mwana wamwamuna wolumala mapazi.+ Mwanayu anali ndi zaka zisanu pamene kunabwera uthenga wa imfa ya Sauli ndi Yonatani kuchokera ku Yezereeli.+ Uthengawu utafika, mlezi wake anamunyamula ndi kuthawa naye. Pamene anali kuthawa mwamantha, mleziyo anagwetsa mwanayo ndipo analumala. Mwanayo dzina lake anali Mefiboseti.+

  • 2 Samueli 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli, atalowa ndi kuonana ndi Davide, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ Pamenepo Davide anati: “Mefiboseti!” Poyankha, iye anati: “Ndine pano mtumiki wanu.”

  • 2 Samueli 19:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma Mefiboseti,+ mdzukulu wake wa Sauli, anabwera kudzaonana ndi mfumu. Iye sanasamalire mapazi ake,+ kumeta ndevu zake zapamlomo+ kapena kuchapa zovala zake kuchokera tsiku limene mfumu inachoka mpaka tsiku limene inabwerera mu mtendere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena