1 Samueli 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ifenso tikufuna kukhala ngati mitundu ina yonse,+ ndipo mfumu yathuyo ndi imene izitiweruza ndi kutitsogolera kukamenya nkhondo zathu.” Mlaliki 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi ya chikondi ndi nthawi ya chidani ndi munthu.+ Nthawi yankhondo+ ndi nthawi yamtendere.+
20 Ifenso tikufuna kukhala ngati mitundu ina yonse,+ ndipo mfumu yathuyo ndi imene izitiweruza ndi kutitsogolera kukamenya nkhondo zathu.”