1 Samueli 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Abigayeli ataona Davide, nthawi yomweyo anatsika mofulumira pabulu wake. Iye anagwada pamaso pa Davide ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ 2 Samueli 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mkazi wa ku Tekowa uja anapita kukaonana ndi mfumu, ndipo anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ kenako anadzigwetsa pansi, n’kunena kuti: “Chonde mfumu, ndipulumutseni!”+
23 Abigayeli ataona Davide, nthawi yomweyo anatsika mofulumira pabulu wake. Iye anagwada pamaso pa Davide ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
4 Pamenepo mkazi wa ku Tekowa uja anapita kukaonana ndi mfumu, ndipo anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ kenako anadzigwetsa pansi, n’kunena kuti: “Chonde mfumu, ndipulumutseni!”+