2 Mafumu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu ya Isiraeli ikuyenda pamwamba pa khoma, mayi wina analankhula mokweza kwa mfumuyo kuti: “Ndithandizeni mbuyanga mfumu!”+ Mateyu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+
26 Mfumu ya Isiraeli ikuyenda pamwamba pa khoma, mayi wina analankhula mokweza kwa mfumuyo kuti: “Ndithandizeni mbuyanga mfumu!”+
9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+