1 Samueli 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ 1 Samueli 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+
8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+