Ekisodo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Munthu akaba ng’ombe kapena nkhosa, n’kuipha kapena kuigulitsa, azilipira ng’ombe zisanu pa ng’ombe imodzi imene waba, ndi nkhosa zinayi pa nkhosa imodzi imene waba.+
22 “Munthu akaba ng’ombe kapena nkhosa, n’kuipha kapena kuigulitsa, azilipira ng’ombe zisanu pa ng’ombe imodzi imene waba, ndi nkhosa zinayi pa nkhosa imodzi imene waba.+